1 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa. Yobu 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ife tabadwa dzulo,+ ndipo sitikudziwa kalikonse,Chifukwa masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi.+ Yobu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amaphuka ngati duwa n’kuthotholedwa.+Amathawa ngati mthunzi+ ndipo sakhalaponso. Salimo 102:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masiku a moyo wanga ali ngati chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa,+Ndipo ndauma ngati udzu.+ Mlaliki 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+
15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa.
9 Pakuti ife tabadwa dzulo,+ ndipo sitikudziwa kalikonse,Chifukwa masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi.+
11 Masiku a moyo wanga ali ngati chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa,+Ndipo ndauma ngati udzu.+
13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+