Yobu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amaphuka ngati duwa n’kuthotholedwa.+Amathawa ngati mthunzi+ ndipo sakhalaponso. Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+