Genesis 48:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maso a Isiraeli anali atafooka chifukwa chokalamba,+ moti sankatha kuona. Yosefe anabweretsa anawo pafupi ndi bambo ake, ndipo bambo akewo anawapsompsona anawo n’kuwakumbatira.+ Mlaliki 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uchite zimenezi kuwala kwa dzuwa, mwezi, ndi nyenyezi kusanazime,+ ndiponso mitambo isanabwerere kuti igwetse mvula. Yohane 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+
10 Maso a Isiraeli anali atafooka chifukwa chokalamba,+ moti sankatha kuona. Yosefe anabweretsa anawo pafupi ndi bambo ake, ndipo bambo akewo anawapsompsona anawo n’kuwakumbatira.+
2 Uchite zimenezi kuwala kwa dzuwa, mwezi, ndi nyenyezi kusanazime,+ ndiponso mitambo isanabwerere kuti igwetse mvula.
18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+