Genesis 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Isaki anakalamba moti maso ake sanali kuonanso.+ Ndiyeno anaitanitsa mwana wake wamkulu Esau,+ n’kumuuza kuti: “Mwana wanga!” Iye anayankha kuti: “Ine bambo!” 1 Samueli 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 (Eli anali ndi zaka 98, ndipo maso ake anangokhala tong’o koma sanali kuona.)+
27 Tsopano Isaki anakalamba moti maso ake sanali kuonanso.+ Ndiyeno anaitanitsa mwana wake wamkulu Esau,+ n’kumuuza kuti: “Mwana wanga!” Iye anayankha kuti: “Ine bambo!”