Genesis 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Isaki anakalamba moti maso ake sanali kuonanso.+ Ndiyeno anaitanitsa mwana wake wamkulu Esau,+ n’kumuuza kuti: “Mwana wanga!” Iye anayankha kuti: “Ine bambo!” Mlaliki 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawi imeneyo oyang’anira nyumba+ azidzanjenjemera, amuna amphamvu adzapindika,+ akazi opera ufa+ adzasiya kugwira ntchito chifukwa adzatsala ochepa, akazi oyang’ana pawindo+ azidzaona mdima,
27 Tsopano Isaki anakalamba moti maso ake sanali kuonanso.+ Ndiyeno anaitanitsa mwana wake wamkulu Esau,+ n’kumuuza kuti: “Mwana wanga!” Iye anayankha kuti: “Ine bambo!”
3 Pa nthawi imeneyo oyang’anira nyumba+ azidzanjenjemera, amuna amphamvu adzapindika,+ akazi opera ufa+ adzasiya kugwira ntchito chifukwa adzatsala ochepa, akazi oyang’ana pawindo+ azidzaona mdima,