2 Samueli 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Afilisiti+ anabwera kudzachita nkhondo ndi Isiraeli. Pamenepo Davide ndi atumiki ake anapita komweko n’kumenyana ndi Afilisiti, ndipo Davide anatopa. Salimo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+ Salimo 90:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti masiku athu onse atha chifukwa cha mkwiyo wanu.+Zaka zathu zafika kumapeto ngati mpweya wotuluka m’mphuno pousa moyo.+ Salimo 102:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Moyo wanga utafika pachimake, anachepetsa mphamvu zanga,+Anafupikitsa masiku a moyo wanga.+
15 Ndiyeno Afilisiti+ anabwera kudzachita nkhondo ndi Isiraeli. Pamenepo Davide ndi atumiki ake anapita komweko n’kumenyana ndi Afilisiti, ndipo Davide anatopa.
15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+
9 Pakuti masiku athu onse atha chifukwa cha mkwiyo wanu.+Zaka zathu zafika kumapeto ngati mpweya wotuluka m’mphuno pousa moyo.+