Genesis 48:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maso a Isiraeli anali atafooka chifukwa chokalamba,+ moti sankatha kuona. Yosefe anabweretsa anawo pafupi ndi bambo ake, ndipo bambo akewo anawapsompsona anawo n’kuwakumbatira.+ Yesaya 59:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tikungoyenda ndi khoma ngati anthu akhungu, ndipo tikungofufuzafufuza ngati anthu opanda maso.+ Tapunthwa masanasana ngati kuti tili mu mdima wamadzulo. Pakati pa anthu ojintcha, tikungokhala ngati anthu akufa.+ Mateyu 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako anawagwira m’maso,+ n’kunena kuti: “Malinga ndi chikhulupiriro chanu zichitike momwemo kwa inu,”
10 Maso a Isiraeli anali atafooka chifukwa chokalamba,+ moti sankatha kuona. Yosefe anabweretsa anawo pafupi ndi bambo ake, ndipo bambo akewo anawapsompsona anawo n’kuwakumbatira.+
10 Tikungoyenda ndi khoma ngati anthu akhungu, ndipo tikungofufuzafufuza ngati anthu opanda maso.+ Tapunthwa masanasana ngati kuti tili mu mdima wamadzulo. Pakati pa anthu ojintcha, tikungokhala ngati anthu akufa.+
29 Kenako anawagwira m’maso,+ n’kunena kuti: “Malinga ndi chikhulupiriro chanu zichitike momwemo kwa inu,”