Mateyu 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Atagwidwa ndi chifundo, Yesu anagwira maso awo.+ Nthawi yomweyo akhunguwo anayamba kuona ndipo anam’tsatira.+
34 Atagwidwa ndi chifundo, Yesu anagwira maso awo.+ Nthawi yomweyo akhunguwo anayamba kuona ndipo anam’tsatira.+