Maliko 10:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Yesu anamuuza kuti: “Pita, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kutsatira Yesu mumsewu.+ Luka 18:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kumutsatira akulemekeza Mulungu.+ Komanso anthu onse, ataona zimenezi, anatamanda Mulungu.
52 Yesu anamuuza kuti: “Pita, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kutsatira Yesu mumsewu.+
43 Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kumutsatira akulemekeza Mulungu.+ Komanso anthu onse, ataona zimenezi, anatamanda Mulungu.