Maliko 10:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Yesu anamuuza kuti: “Pita, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kutsatira Yesu mumsewu.+
52 Yesu anamuuza kuti: “Pita, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kutsatira Yesu mumsewu.+