-
Maliko 8:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Pamenepo anagwiranso m’maso mwa munthuyo. Munthuyo anayamba kuona bwinobwino, chifukwa anam’chiritsa, moti anayamba kuona chilichonse bwinobwino.
-