Salimo 146:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+ Yesaya 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu akhungu ndidzawayendetsa m’njira imene sakuidziwa.+ Ndidzawadutsitsa mumsewu umene sakuudziwa.+ Malo amdima ndidzawasandutsa kuwala pamaso pawo,+ ndipo malo okumbikakumbika ndidzawasalaza.+ Zimenezi ndi zimene ndidzawachitire ndipo sindidzawasiya.”+ Mateyu 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ndipo maso awo anatseguka. Chotero Yesu anawalamula mwamphamvu kuti: “Samalani, aliyense asadziwe zimenezi.”+
8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+
16 Anthu akhungu ndidzawayendetsa m’njira imene sakuidziwa.+ Ndidzawadutsitsa mumsewu umene sakuudziwa.+ Malo amdima ndidzawasandutsa kuwala pamaso pawo,+ ndipo malo okumbikakumbika ndidzawasalaza.+ Zimenezi ndi zimene ndidzawachitire ndipo sindidzawasiya.”+
30 ndipo maso awo anatseguka. Chotero Yesu anawalamula mwamphamvu kuti: “Samalani, aliyense asadziwe zimenezi.”+