Salimo 94:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova sadzataya anthu ake,+Kapena kusiya cholowa chake.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+