Yesaya 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 “Imirira+ mkazi iwe! Onetsa kuwala kwako,+ pakuti kuwala kwako kwafika,+ ndipo ulemerero wa Yehova wakuunika.+ Yesaya 60:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+
60 “Imirira+ mkazi iwe! Onetsa kuwala kwako,+ pakuti kuwala kwako kwafika,+ ndipo ulemerero wa Yehova wakuunika.+
20 Dzuwa lako silidzalowanso, ndipo mwezi wako sudzapitanso kumdima. Pakuti kwa iwe, Yehova adzakhala kuwala kosatha mpaka kalekale,+ ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+