Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+ Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+
17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+