Yesaya 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+ Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba. Aefeso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti poyamba munali mdima,+ koma tsopano ndinu kuwala+ mogwirizana ndi Ambuye. Yendanibe ngati ana a kuwala. Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+
6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+
16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba.
8 Pakuti poyamba munali mdima,+ koma tsopano ndinu kuwala+ mogwirizana ndi Ambuye. Yendanibe ngati ana a kuwala.
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+