Yesaya 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye sadzafuula kapena kukweza mawu ake, ndipo mawu ake sadzamvedwa mumsewu.+ Mateyu 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma anawalamula mwamphamvu kuti asamuulule.+ Maliko 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe+ ndipo ukapereke zinthu zimene Mose analamula+ chifukwa cha kuyeretsedwa kwako, kuti zikhale umboni kwa iwo.”+ Luka 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+
44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe+ ndipo ukapereke zinthu zimene Mose analamula+ chifukwa cha kuyeretsedwa kwako, kuti zikhale umboni kwa iwo.”+
14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+