Mateyu 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yesu anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi,+ koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke mphatso+ imene Mose analamula, kuti ikhale umboni kwa iwo.” Maliko 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe+ ndipo ukapereke zinthu zimene Mose analamula+ chifukwa cha kuyeretsedwa kwako, kuti zikhale umboni kwa iwo.”+
4 Ndiyeno Yesu anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi,+ koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke mphatso+ imene Mose analamula, kuti ikhale umboni kwa iwo.”
44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe+ ndipo ukapereke zinthu zimene Mose analamula+ chifukwa cha kuyeretsedwa kwako, kuti zikhale umboni kwa iwo.”+