Mateyu 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ndipo maso awo anatseguka. Chotero Yesu anawalamula mwamphamvu kuti: “Samalani, aliyense asadziwe zimenezi.”+ Mateyu 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma anawalamula mwamphamvu kuti asamuulule.+ Maliko 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimenezo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, m’pamenenso iwo anali kuzifalitsa kwambiri.+ Luka 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+
30 ndipo maso awo anatseguka. Chotero Yesu anawalamula mwamphamvu kuti: “Samalani, aliyense asadziwe zimenezi.”+
36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimenezo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, m’pamenenso iwo anali kuzifalitsa kwambiri.+
14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+