Maliko 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimenezo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, m’pamenenso iwo anali kuzifalitsa kwambiri.+ Luka 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Pamenepo, makolo akewo anakondwa kwambiri, koma Yesu anawalangiza kuti asauze aliyense zimene zachitikazo.+
36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimenezo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, m’pamenenso iwo anali kuzifalitsa kwambiri.+
56 Pamenepo, makolo akewo anakondwa kwambiri, koma Yesu anawalangiza kuti asauze aliyense zimene zachitikazo.+