Maliko 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimenezo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, m’pamenenso iwo anali kuzifalitsa kwambiri.+ Luka 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+
36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimenezo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, m’pamenenso iwo anali kuzifalitsa kwambiri.+
14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+