Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 wansembe azim’lamula kuti atenge zofunika pa kudziyeretsa kwake. Azitenga mbalame zamoyo ziwiri zosadetsedwa,+ nthambi ya mtengo wa mkungudza,+ ulusi wofiira kwambiri+ ndi kamtengo ka hisope.+

  • Levitiko 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiyeno wansembe azipereka nsembe yopsereza ndi nsembe yambewu+ paguwa lansembe. Akatero, wansembe+ azim’phimbira machimo,+ ndipo munthuyo azikhala woyera.+

  • Maliko 1:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe+ ndipo ukapereke zinthu zimene Mose analamula+ chifukwa cha kuyeretsedwa kwako, kuti zikhale umboni kwa iwo.”+

  • Luka 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense.+ Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke nsembe+ ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira, kuti ikhale umboni kwa iwo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena