Levitiko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+ Levitiko 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Kenako wansembe azipereka mmodzi mwa ana a njiwa kapena m’modzi mwa ana a nkhunda, malinga ndi zimene munthuyo angakwanitse.+ Levitiko 14:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiyeno kuti achite mwambo woyeretsa nyumbayo, azitenga mbalame ziwiri,+ nthambi ya mtengo wa mkungudza,+ ulusi wofiira kwambiri+ ndi kamtengo ka hisope.
14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+
30 “Kenako wansembe azipereka mmodzi mwa ana a njiwa kapena m’modzi mwa ana a nkhunda, malinga ndi zimene munthuyo angakwanitse.+
49 Ndiyeno kuti achite mwambo woyeretsa nyumbayo, azitenga mbalame ziwiri,+ nthambi ya mtengo wa mkungudza,+ ulusi wofiira kwambiri+ ndi kamtengo ka hisope.