Luka 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kumeneko iwo anapereka nsembe malinga ndi zimene chilamulo cha Yehova chimanena kuti: “Njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.”+
24 Kumeneko iwo anapereka nsembe malinga ndi zimene chilamulo cha Yehova chimanena kuti: “Njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.”+