Levitiko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+ Levitiko 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Koma ngati sangakwanitse kupereka nkhosa,+ azibweretsa kwa Yehova njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda kuti zikhale nsembe za kupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza. Levitiko 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati sangakwanitse kupeza nkhosa, azipereka njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.+ Mbalame imodzi ikhale nsembe yopsereza, inayo ikhale nsembe yamachimo. Pamenepo wansembe azim’phimbira machimo+ ndipo mkaziyo azikhala woyera.’”
14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+
7 “‘Koma ngati sangakwanitse kupereka nkhosa,+ azibweretsa kwa Yehova njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda kuti zikhale nsembe za kupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.
8 Koma ngati sangakwanitse kupeza nkhosa, azipereka njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.+ Mbalame imodzi ikhale nsembe yopsereza, inayo ikhale nsembe yamachimo. Pamenepo wansembe azim’phimbira machimo+ ndipo mkaziyo azikhala woyera.’”