Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+

  • Levitiko 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Koma ngati sangakwanitse kupereka nkhosa,+ azibweretsa kwa Yehova njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda kuti zikhale nsembe za kupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.

  • Levitiko 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.

  • Luka 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kumeneko iwo anapereka nsembe malinga ndi zimene chilamulo cha Yehova chimanena kuti: “Njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena