Levitiko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+ Levitiko 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda ndipo azibwera nazo pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako, ndi kupereka mbalamezo kwa wansembe.
14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+
14 Pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda ndipo azibwera nazo pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako, ndi kupereka mbalamezo kwa wansembe.