Levitiko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+ Levitiko 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza. Numeri 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo pa tsiku la 8, abweretse ana a njiwa awiri, kapena ana a nkhunda awiri kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+
14 “‘Koma ngati akupereka mbalame kuti ikhale nsembe yake yopsereza kwa Yehova, azipereka njiwa+ kapena ana a nkhunda.+
22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.
10 Ndipo pa tsiku la 8, abweretse ana a njiwa awiri, kapena ana a nkhunda awiri kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+