-
Numeri 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndipo pa tsiku la 8, azibweretsa njiwa ziwiri kapena ana a nkhunda awiri kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.
-