Numeri 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo pa tsiku la 8, abweretse ana a njiwa awiri, kapena ana a nkhunda awiri kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+
10 Ndipo pa tsiku la 8, abweretse ana a njiwa awiri, kapena ana a nkhunda awiri kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako.+