Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ngati sangakwanitse kupeza nkhosa, azipereka njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.+ Mbalame imodzi ikhale nsembe yopsereza, inayo ikhale nsembe yamachimo. Pamenepo wansembe azim’phimbira machimo+ ndipo mkaziyo azikhala woyera.’”

  • Levitiko 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Koma ngati munthuyo ali wosauka+ ndipo sangakwanitse kupeza zinthu zimenezi,+ azibweretsa nkhosa yaing’ono yamphongo imodzi monga nsembe ya kupalamula. Nsembeyo aziiweyulira uku ndi uku kuti am’phimbire machimo. Azibweretsanso muyezo umodzi wa mafuta ndi ufa wosalala wothira mafuta. Ufawo uzikhala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa, monga nsembe yake yambewu.

  • 2 Akorinto 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.

  • Yakobo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tamverani abale anga okondedwa. Mulungu anasankha anthu amene ali osauka+ m’dzikoli kuti akhale olemera+ m’chikhulupiriro ndi olandira cholowa cha ufumu umene anaulonjeza kwa omukonda,+ sanatero kodi?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena