Salimo 72:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adzamvera chisoni munthu wonyozeka ndi wosauka,+Ndipo adzapulumutsa miyoyo ya anthu osauka.+ Miyambo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wonyoza munthu wosauka amanyoza amene anam’panga.+ Amene amasangalala ndi tsoka la wina sadzalephera kulangidwa.+ Miyambo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wolemera ndiponso munthu wosauka n’chimodzimodzi.+ Amene anapanga onsewa ndi Yehova.+ Luka 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo anakweza maso ake ndi kuyang’ana ophunzira ake, ndipo anawauza kuti:+ “Odala ndinu osaukanu,+ chifukwa ufumu wa Mulungu ndi wanu.
5 Wonyoza munthu wosauka amanyoza amene anam’panga.+ Amene amasangalala ndi tsoka la wina sadzalephera kulangidwa.+
20 Pamenepo anakweza maso ake ndi kuyang’ana ophunzira ake, ndipo anawauza kuti:+ “Odala ndinu osaukanu,+ chifukwa ufumu wa Mulungu ndi wanu.