Luka 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako anayangʼana ophunzira ake nʼkuyamba kuwauza kuti: “Osaukanu ndinu osangalala, chifukwa Ufumu wa Mulungu ndi wanu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:20 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, ptsa. 10-112/15/1987, tsa. 9
20 Kenako anayangʼana ophunzira ake nʼkuyamba kuwauza kuti: “Osaukanu ndinu osangalala, chifukwa Ufumu wa Mulungu ndi wanu.+