Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ngati wolonjezayo ndi wosauka moti sangakwanitse mtengo woikidwiratuwo,+ azikaonetsa munthu woperekedwayo kwa wansembe, ndipo wansembe azinena mtengo wa munthuyo.+ Wansembe adzanena mtengo umene wolonjezayo angakwanitse.+

  • Deuteronomo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+

  • Deuteronomo 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mphatso yochokera m’manja mwa aliyense izikhala yolingana ndi madalitso amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+

  • Miyambo 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+

  • Maliko 12:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Choncho Yesu anaitana ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mkazi wamasiye wosaukayu waponya zochuluka kuposa onse amene aponya ndalama moponya zoperekamo.+

  • Luka 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo iye anati: “Kunena zoona, Mkazi wamasiyeyu, ngakhale kuti ndi wosauka, waponya zochuluka kuposa onse amene aponya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena