1 Mbiri 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+ Luka 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo iye anati: “Kunena zoona, Mkazi wamasiyeyu, ngakhale kuti ndi wosauka, waponya zochuluka kuposa onse amene aponya.+ 2 Akorinto 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.
9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+
3 Ndipo iye anati: “Kunena zoona, Mkazi wamasiyeyu, ngakhale kuti ndi wosauka, waponya zochuluka kuposa onse amene aponya.+
12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.