-
1 Akorinto 16:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tsiku lililonse loyamba la mlungu, aliyense wa inu aziika kenakake pambali kunyumba kwake malinga ndi mmene zinthu zikuyendera pa moyo wake, kuti ndikadzafika, zopereka zisadzaperekedwe pa nthawi imeneyo.
-