-
1 Akorinto 16:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tsiku loyamba la mlungu uliwonse, aliyense aziika kenakake pambali kunyumba kwake mogwirizana ndi zimene angakwanitse, kuti zopereka zisadzaperekedwe nditafika.
-