Deuteronomo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+ 2 Akorinto 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.
10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+
12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.