Luka 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anaona mkazi wina wamasiye wosauka akuponya timakobidi tiwiri tating’ono mmenemo.+ 2 Akorinto 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.
12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.