Levitiko 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza. Luka 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kumeneko iwo anapereka nsembe malinga ndi zimene chilamulo cha Yehova chimanena kuti: “Njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.”+
22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.
24 Kumeneko iwo anapereka nsembe malinga ndi zimene chilamulo cha Yehova chimanena kuti: “Njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda.”+