Yesaya 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chigwa chilichonse chikwezedwe m’mwamba,+ ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe.+ Malo okumbikakumbika asalazidwe ndipo malo azitundazitunda akhale chigwa.+ Luka 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzenje lililonse likwiriridwe, ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zisalazidwe. Njira zokhotakhota zikhale zowongoka ndipo malo okumbikakumbika akhale osalala bwino.+
4 Chigwa chilichonse chikwezedwe m’mwamba,+ ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe.+ Malo okumbikakumbika asalazidwe ndipo malo azitundazitunda akhale chigwa.+
5 Dzenje lililonse likwiriridwe, ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zisalazidwe. Njira zokhotakhota zikhale zowongoka ndipo malo okumbikakumbika akhale osalala bwino.+