Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 29:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 M’tsiku limenelo, ogontha adzamva mawu a m’buku.+ Ngakhale maso a anthu akhungu adzamasuka ku mdima wandiweyani ndipo adzayamba kuona.+

  • Yeremiya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Kodi ndilankhule ndi ndani ndipo ndichenjeze ndani kuti amve? Taonani! Makutu awo sanawachite mdulidwe, moti sangamve.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala onyozeka kwa iwo,+ ndipo sakukondwera nawo.+

  • Maliko 7:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Atatero, makutu ake anatseguka,+ lilime lake lomangikalo linamasuka, moti anayamba kulankhula bwinobwino.

  • Luka 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho poyankha anauza amuna awiri aja kuti: “Pitani+ mukamuuze Yohane zimene mwaona ndi kumva: Akhungu+ akuona, olumala akuyenda, akhate akuyeretsedwa, ogontha akumva, akufa akuukitsidwa ndipo aumphawi akumva+ uthenga wabwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena