Yesaya 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu akhungu adzatsegulidwa,+ ndipo makutu a anthu ogontha adzayamba kumva.+ Mateyu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+ Mateyu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anthu ochuluka anakhamukira kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, akhungu, osalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana, moti anawakhazika pamapazi ake mochita ngati akum’ponyera, ndipo anawachiritsa onsewo.+
5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu akhungu adzatsegulidwa,+ ndipo makutu a anthu ogontha adzayamba kumva.+
5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+
30 Kenako anthu ochuluka anakhamukira kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, akhungu, osalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana, moti anawakhazika pamapazi ake mochita ngati akum’ponyera, ndipo anawachiritsa onsewo.+