Mateyu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene anali ndi vuto losaona akuona,+ olumala akuyenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo amene anali ndi vuto losamva akumva. Akufa akuukitsidwa ndipo osauka akuuzidwa uthenga wabwino.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 96 Nsanja ya Olonda,7/1/1997, tsa. 61/1/1987, ptsa. 8-9
5 Amene anali ndi vuto losaona akuona,+ olumala akuyenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo amene anali ndi vuto losamva akumva. Akufa akuukitsidwa ndipo osauka akuuzidwa uthenga wabwino.+