Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 35:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzatsegulidwa,+

      Ndipo makutu a anthu amene ali ndi vuto losamva adzayamba kumva.+

       6 Pa nthawi imeneyo, munthu wolumala adzadumpha ngati mmene imachitira mbawala,+

      Ndipo lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mosangalala.+

      Mʼchipululu mudzatumphuka madzi,

      Ndipo mʼdera lachipululu mudzayenda mitsinje.

  • Yesaya 61:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Mzimu wa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, uli pa ine,+

      Chifukwa Yehova anandidzoza kuti ndilengeze uthenga wabwino kwa anthu ofatsa.+

      Anandituma kuti ndikamange mabala a anthu osweka mtima,

      Kuti ndilengeze za ufulu kwa anthu amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,

      Komanso kuti maso a akaidi adzatsegulidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena