Mateyu 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Atagwidwa ndi chifundo, Yesu anagwira maso awo.+ Nthawi yomweyo akhunguwo anayamba kuona ndipo anam’tsatira.+ Luka 18:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kumutsatira akulemekeza Mulungu.+ Komanso anthu onse, ataona zimenezi, anatamanda Mulungu.
34 Atagwidwa ndi chifundo, Yesu anagwira maso awo.+ Nthawi yomweyo akhunguwo anayamba kuona ndipo anam’tsatira.+
43 Nthawi yomweyo anayamba kuona,+ ndipo anayamba kumutsatira akulemekeza Mulungu.+ Komanso anthu onse, ataona zimenezi, anatamanda Mulungu.