Luka 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo anthu onsewo anadabwa kwambiri,+ ndipo anayamba kutamanda Mulungu, mwakuti anagwidwa ndi mantha. Iwo anali kunena kuti: “Taona zodabwitsa lero!”+ Machitidwe 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho atawonjezera kuwaopseza, anawamasula, pakuti sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso anaopa anthu,+ pakuti onse anali kutamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo. Agalatiya 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anthuwo anayamba kulemekeza+ Mulungu chifukwa cha ine.
26 Pamenepo anthu onsewo anadabwa kwambiri,+ ndipo anayamba kutamanda Mulungu, mwakuti anagwidwa ndi mantha. Iwo anali kunena kuti: “Taona zodabwitsa lero!”+
21 Choncho atawonjezera kuwaopseza, anawamasula, pakuti sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso anaopa anthu,+ pakuti onse anali kutamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo.