Maliko 5:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Nthawi yomweyo kamtsikanako kanadzuka ndi kuyamba kuyenda. Mwanayo anali ndi zaka 12. Pamenepo anthuwo anasangalala kwambiri.+ Machitidwe 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako anayamba kumuzindikira kuti ndi mwamuna amene anali kukhala pa Chipata Chokongola+ cha kachisi n’kumapempha mphatso zachifundo. Ndipo iwo anadabwa ndi kuzizwa kwambiri+ ndi zimene zinam’chitikirazo.
42 Nthawi yomweyo kamtsikanako kanadzuka ndi kuyamba kuyenda. Mwanayo anali ndi zaka 12. Pamenepo anthuwo anasangalala kwambiri.+
10 Kenako anayamba kumuzindikira kuti ndi mwamuna amene anali kukhala pa Chipata Chokongola+ cha kachisi n’kumapempha mphatso zachifundo. Ndipo iwo anadabwa ndi kuzizwa kwambiri+ ndi zimene zinam’chitikirazo.