Deuteronomo 28:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+ Miyambo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+ 1 Yohane 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma amene amadana ndi m’bale wake ndiye kuti ali mu mdima ndipo akuyenda mu mdimawo,+ ndiponso sakudziwa kumene akupita+ chifukwa maso ake achita khungu chifukwa cha mdimawo.
29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+
11 Koma amene amadana ndi m’bale wake ndiye kuti ali mu mdima ndipo akuyenda mu mdimawo,+ ndiponso sakudziwa kumene akupita+ chifukwa maso ake achita khungu chifukwa cha mdimawo.