Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo ana a Isiraeli anatumikira Egiloni, mfumu ya Mowabu zaka 18.+

  • Oweruza 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anali kuwazungulira ndi kuwawonongera zokolola zawo zonse mpaka kukafika ku Gaza. Sanali kuwasiyira chakudya chilichonse ngakhalenso nkhosa, ng’ombe kapena bulu mu Isiraeli.+

  • Nehemiya 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chifukwa chochita zimenezi, munawapereka m’manja mwa adani awo+ amene anapitiriza kuwasautsa.+ Koma akakumana ndi nsautso, anali kukulirirani,+ ndipo inu munali kumva muli kumwambako.+ Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu,+ munali kuwapatsa owapulumutsa+ amene anali kuwalanditsa m’manja mwa adani awo.+

  • Salimo 106:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Ndi kuti adani awowo awapondereze,

      Komanso kuti awagonjetse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena